10 Mogwirizana ndi kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu anandisonyeza, ndinayala maziko+ ngati mmene amachitira munthu waluso pa ntchito zomangamanga. Koma amene akumanga pamaziko amenewo ndi munthu wina. Choncho aliyense asamale mmene akumangirapo.