1 Akorinto 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati munthu wina wawononga kachisi wa Mulungu, Mulungu adzamuwononga munthuyo, chifukwa kachisi wa Mulungu ndi woyera, ndipo kachisiyo ndi inuyo.+
17 Ngati munthu wina wawononga kachisi wa Mulungu, Mulungu adzamuwononga munthuyo, chifukwa kachisi wa Mulungu ndi woyera, ndipo kachisiyo ndi inuyo.+