1 Akorinto 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu asamadzinamize. Ngati aliyense wa inu akuganiza kuti ndi wanzeru nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:18 Nsanja ya Olonda,9/15/1992, tsa. 24
18 Munthu asamadzinamize. Ngati aliyense wa inu akuganiza kuti ndi wanzeru nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru.