1 Akorinto 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi akukupangitsa kukhala wosiyana ndi ena ndi ndani? Ndipo uli ndi chiyani chimene sunachite kulandira?+ Ndiye ngati unachita kulandira zinthu zimenezo, nʼchifukwa chiyani ukudzitama ngati kuti sunachite kulandira?
7 Kodi akukupangitsa kukhala wosiyana ndi ena ndi ndani? Ndipo uli ndi chiyani chimene sunachite kulandira?+ Ndiye ngati unachita kulandira zinthu zimenezo, nʼchifukwa chiyani ukudzitama ngati kuti sunachite kulandira?