1 Akorinto 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Yehova* akalola ndibwera posachedwapa, ndipo sindidzafuna kumva mawu awo odzikuzawo, koma ndidzafuna ndione mphamvu zawo.
19 Koma Yehova* akalola ndibwera posachedwapa, ndipo sindidzafuna kumva mawu awo odzikuzawo, koma ndidzafuna ndione mphamvu zawo.