1 Akorinto 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mbiri yamvekatu kuti pakati panu pakuchitika chiwerewere*+ ndipo chiwerewere chake ndi choti ngakhale anthu a mitundu ina sachita. Akuti mwamuna wina watengana ndi mkazi wa bambo ake.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Nsanja ya Olonda,8/15/1997, tsa. 28
5 Mbiri yamvekatu kuti pakati panu pakuchitika chiwerewere*+ ndipo chiwerewere chake ndi choti ngakhale anthu a mitundu ina sachita. Akuti mwamuna wina watengana ndi mkazi wa bambo ake.+