1 Akorinto 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kudzitama kwanu si kwabwino. Kodi simukudziwa kuti zofufumitsa zapangʼono zimafufumitsa mtanda wonse wa ufa wokandakanda?+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 57 Nsanja ya Olonda,3/15/1993, tsa. 5
6 Kudzitama kwanu si kwabwino. Kodi simukudziwa kuti zofufumitsa zapangʼono zimafufumitsa mtanda wonse wa ufa wokandakanda?+