1 Akorinto 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho tiyeni tichite Chikondwerero cha Pasikachi,+ osati ndi zofufumitsa zakale, kapena zofufumitsa zoimira zoipa ndi uchimo, koma ndi mkate wopanda zofufumitsa woimira kuona mtima ndi choonadi. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:8 Nsanja ya Olonda,3/15/1993, tsa. 5
8 Choncho tiyeni tichite Chikondwerero cha Pasikachi,+ osati ndi zofufumitsa zakale, kapena zofufumitsa zoimira zoipa ndi uchimo, koma ndi mkate wopanda zofufumitsa woimira kuona mtima ndi choonadi.