1 Akorinto 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mʼkalata yanga, ndinakulemberani kuti musiye kugwirizana ndi anthu achiwerewere.*