1 Akorinto 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sindikutanthauza kuti muzipeweratu anthu achiwerewere* amʼdzikoli+ kapenanso adyera, olanda ndi opembedza mafano. Kuti muchite zimenezo, ndiye mungafunike kutuluka mʼdzikoli.+
10 Sindikutanthauza kuti muzipeweratu anthu achiwerewere* amʼdzikoli+ kapenanso adyera, olanda ndi opembedza mafano. Kuti muchite zimenezo, ndiye mungafunike kutuluka mʼdzikoli.+