1 Akorinto 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho, ngati muli ndi nkhani zamʼmoyo uno zofunika kuweruza,+ kodi mukupereka udindo woweruza kwa anthu amene mpingo sungawadalire? 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:4 Nsanja ya Olonda,10/15/1995, tsa. 20
4 Choncho, ngati muli ndi nkhani zamʼmoyo uno zofunika kuweruza,+ kodi mukupereka udindo woweruza kwa anthu amene mpingo sungawadalire?