-
1 Akorinto 6:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndikulankhula zimenezi kuti ndikuchititseni manyazi. Kodi pakati panu palibe wanzeru ndi mmodzi yemwe amene angaweruze milandu ya abale ake?
-