1 Akorinto 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zinthu zonse ndi zololeka kwa ine, koma si zonse zimene zili zaphindu.+ Zinthu zonse ndi zololeka kwa ine, koma sindidzalola kuti chinthu china chizindilamulira. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:12 Mawu a Mulungu, tsa. 166
12 Zinthu zonse ndi zololeka kwa ine, koma si zonse zimene zili zaphindu.+ Zinthu zonse ndi zololeka kwa ine, koma sindidzalola kuti chinthu china chizindilamulira.