1 Akorinto 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chakudya ndi cha mimba, ndipo mimba ndi ya chakudya, koma Mulungu adzawononga mimba ndi chakudya chomwe.+ Thupi si lochitira chiwerewere,* koma ndi la Ambuye+ ndipo Ambuye ndi amene amapereka zofunika mʼthupi.
13 Chakudya ndi cha mimba, ndipo mimba ndi ya chakudya, koma Mulungu adzawononga mimba ndi chakudya chomwe.+ Thupi si lochitira chiwerewere,* koma ndi la Ambuye+ ndipo Ambuye ndi amene amapereka zofunika mʼthupi.