1 Akorinto 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi inu simukudziwa kuti amene wagonana ndi hule amakhala thupi limodzi ndi huleyo? Chifukwa anati, “Awiriwo adzakhala thupi limodzi.”+
16 Kodi inu simukudziwa kuti amene wagonana ndi hule amakhala thupi limodzi ndi huleyo? Chifukwa anati, “Awiriwo adzakhala thupi limodzi.”+