-
1 Akorinto 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Musamakanizane, pokhapokha ngati mwagwirizana kudikira kaye kwa nthawi inayake kuti mugwiritse ntchito nthawi imeneyo popemphera, kenako nʼkuyambiranso mwa nthawi zonse, kuopera kuti Satana angapitirize kukuyesani mukalephera kudziletsa.
-