1 Akorinto 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ndikanakonda amuna onse akanakhala ngati ineyo. Komabe aliyense ali ndi mphatso+ imene Mulungu anamupatsa ndipo timamutumikira mʼnjira zosiyanasiyana. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:7 Nsanja ya Olonda,10/15/1996, tsa. 11 Galamukani!,2/8/1995, tsa. 15
7 Koma ndikanakonda amuna onse akanakhala ngati ineyo. Komabe aliyense ali ndi mphatso+ imene Mulungu anamupatsa ndipo timamutumikira mʼnjira zosiyanasiyana.