1 Akorinto 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngakhale zili choncho, munthu aliyense akhale mmene analili pamene Yehova* Mulungu ankamuitana.+ Amenewa ndi malangizo amene ndikupereka kumipingo yonse.
17 Ngakhale zili choncho, munthu aliyense akhale mmene analili pamene Yehova* Mulungu ankamuitana.+ Amenewa ndi malangizo amene ndikupereka kumipingo yonse.