-
1 Akorinto 7:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Ndikunenatu zimenezi kuti ndikuthandizeni, osati kuti ndikupanikizeni, koma kuti ndikulimbikitseni kuchita zoyenera ndiponso kutumikira Ambuye nthawi zonse popanda zosokoneza.
-