1 Akorinto 7:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma ngati wina watsimikiza mumtima mwake kuti akhoza kukhala wosakwatira ndipo akutha kulamulira maganizo ake komanso wasankha mumtima mwake kukhalabe wosakwatira,* wachita bwino.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:37 Nsanja ya Olonda,10/15/2011, tsa. 1711/15/1987, ptsa. 13-14
37 Koma ngati wina watsimikiza mumtima mwake kuti akhoza kukhala wosakwatira ndipo akutha kulamulira maganizo ake komanso wasankha mumtima mwake kukhalabe wosakwatira,* wachita bwino.+