1 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano si kanthu+ ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+
4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano si kanthu+ ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+