1 Akorinto 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu amati pali milungu yambiri, kaya kumwamba kapena padziko lapansi.+ Choncho kwa anthu amenewo palidi milungu yambiri ndi ambuye ambiri. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:5 Nsanja ya Olonda,1/1/1992, ptsa. 3-412/1/1990, ptsa. 3-5
5 Anthu amati pali milungu yambiri, kaya kumwamba kapena padziko lapansi.+ Choncho kwa anthu amenewo palidi milungu yambiri ndi ambuye ambiri.