1 Akorinto 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma chakudya sichingatithandize kuyandikira Mulungu.+ Ngati sitinadye chakudyacho, sikuti talakwa, ndipo ngati tadya, sikuti ndife abwino kwambiri kwa iyeyo.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:8 Nsanja ya Olonda,11/15/1989, tsa. 14
8 Koma chakudya sichingatithandize kuyandikira Mulungu.+ Ngati sitinadye chakudyacho, sikuti talakwa, ndipo ngati tadya, sikuti ndife abwino kwambiri kwa iyeyo.+