-
1 Akorinto 8:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ngati wina angaone iweyo wodziwa zinthuwe ukudya chakudya mʼkachisi wa mafano, kodi chikumbumtima cha munthu wofookayo sichidzamulimbikitsa kudya zakudya zoperekedwa kwa mafano?
-