1 Akorinto 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho kudziwa zinthu kwako kungachititse kuti uwononge munthu wofookayo, yemwe ndi mʼbale wako amene Khristu anamufera.+
11 Choncho kudziwa zinthu kwako kungachititse kuti uwononge munthu wofookayo, yemwe ndi mʼbale wako amene Khristu anamufera.+