1 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi alipo msilikali amene amatumikira, koma nʼkumadzilipira yekha? Ndani amalima munda wa mpesa koma osadya zipatso zake?+ Kapena ndani amaweta ziweto koma osamwa mkaka wake?
7 Kodi alipo msilikali amene amatumikira, koma nʼkumadzilipira yekha? Ndani amalima munda wa mpesa koma osadya zipatso zake?+ Kapena ndani amaweta ziweto koma osamwa mkaka wake?