-
1 Akorinto 9:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kapena kodi ananena mawu amenewa poganizira ifeyo? Mawu amenewa anawalembadi poganizira ifeyo, chifukwa wolima ndiponso wopuntha mbewu ayenera kugwira ntchito ndi chiyembekezo choti alandira kenakake.
-