1 Akorinto 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngati tinakupatsani zinthu zauzimu,* kodi nʼkulakwa kulandira* zinthu zofunika pa moyo kuchokera kwa inu?+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:11 Nsanja ya Olonda,12/1/1989, tsa. 27
11 Ngati tinakupatsani zinthu zauzimu,* kodi nʼkulakwa kulandira* zinthu zofunika pa moyo kuchokera kwa inu?+