15 Koma sindinagwiritsepo ntchito ufulu umenewu.+ Ndiponso sikuti ndalemba zimenezi kuti ndiyambe kugwiritsa ntchito ufuluwu, chifukwa zingakhale bwino kuti ineyo ndife, kusiyana nʼkuti . . . palibe munthu amene angandilande zifukwa zomwe ndikudzitamira!+