1 Akorinto 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati ndikulalikira uthenga wabwino, chimenecho si chifukwa chodzitamira, chifukwa ndinalamulidwa kuchita zimenezi. Tsoka kwa ine ngati sindilalikira uthenga wabwino.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:16 Galamukani!,8/8/2001, tsa. 20 Nsanja ya Olonda,9/15/1996, ptsa. 17-18
16 Ngati ndikulalikira uthenga wabwino, chimenecho si chifukwa chodzitamira, chifukwa ndinalamulidwa kuchita zimenezi. Tsoka kwa ine ngati sindilalikira uthenga wabwino.+