1 Akorinto 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndikamachita zimenezi mwa kufuna kwanga, ndidzalandira mphoto. Koma ngakhale nditachita mokakamizika, ndinebe woyangʼanira mogwirizana ndi udindo umene ndinapatsidwa.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:17 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2024, ptsa. 11-12
17 Ndikamachita zimenezi mwa kufuna kwanga, ndidzalandira mphoto. Koma ngakhale nditachita mokakamizika, ndinebe woyangʼanira mogwirizana ndi udindo umene ndinapatsidwa.+