-
1 Akorinto 9:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiye kodi mphoto yanga nʼchiyani? Ndi yakuti ndikamalalikira uthenga wabwino ndiziulalikira kwaulere, kuti ndisagwiritse ntchito molakwa ufulu wanga pa zinthu zokhudza uthenga wabwino.
-