1 Akorinto 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kwa Ayuda ndinakhala ngati Myuda, kuti ndithandize Ayuda.+ Kwa anthu otsatira Chilamulo ndinakhala ngati wotsatira Chilamulo kuti ndithandize anthu otsatira chilamulo, ngakhale kuti sinditsatira Chilamulo.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:20 Nsanja ya Olonda,11/15/1989, tsa. 11
20 Kwa Ayuda ndinakhala ngati Myuda, kuti ndithandize Ayuda.+ Kwa anthu otsatira Chilamulo ndinakhala ngati wotsatira Chilamulo kuti ndithandize anthu otsatira chilamulo, ngakhale kuti sinditsatira Chilamulo.+