1 Akorinto 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndimachita zinthu zonse chifukwa cha uthenga wabwino, kuti ndilalikire uthengawu kwa anthu ena.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:23 Nsanja ya Olonda,11/15/1989, ptsa. 10-14