1 Akorinto 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo onse ankamwa madzi auzimu ofanana.+ Chifukwa ankamwa pathanthwe lauzimu limene linkawatsatira, ndipo thanthwelo linali* Khristu.+
4 Ndipo onse ankamwa madzi auzimu ofanana.+ Chifukwa ankamwa pathanthwe lauzimu limene linkawatsatira, ndipo thanthwelo linali* Khristu.+