1 Akorinto 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taganizirani zimene Aisiraeli* amachita: Kodi amene amadya zinthu zoperekedwa paguwa la nsembe si ndiye kuti amakhala ngati akudya ndi Mulungu?+
18 Taganizirani zimene Aisiraeli* amachita: Kodi amene amadya zinthu zoperekedwa paguwa la nsembe si ndiye kuti amakhala ngati akudya ndi Mulungu?+