1 Akorinto 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kapena ‘kodi tikufuna kuti Yehova* achite nsanje?’+ Kodi mphamvu zathu zingapose mphamvu zake? 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:22 Nsanja ya Olonda,3/1/1987, ptsa. 6-7