-
1 Akorinto 10:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ngati munthu wosakhulupirira wakuitanani ndipo mukufuna kupita, kadyeni chilichonse chimene wakupatsani muli ndi chikumbumtima chabwino ndipo musafunse mafunso.
-