1 Akorinto 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Zimenezi ndi zimene inenso ndikuyesetsa kuchita. Ndikuyesetsa kusangalatsa anthu onse pa zonse zimene ndikuchita. Sindikufuna zopindulitsa ine ndekha,+ koma zopindulitsa anthu ambiri kuti apulumutsidwe.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:33 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 52
33 Zimenezi ndi zimene inenso ndikuyesetsa kuchita. Ndikuyesetsa kusangalatsa anthu onse pa zonse zimene ndikuchita. Sindikufuna zopindulitsa ine ndekha,+ koma zopindulitsa anthu ambiri kuti apulumutsidwe.+