1 Akorinto 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ngati wina ali ndi njala, adye kunyumba, kuti mukasonkhana musaweruzidwe.+ Koma nkhani zimene zatsala ndidzaziona ndikabwera.
34 Ngati wina ali ndi njala, adye kunyumba, kuti mukasonkhana musaweruzidwe.+ Koma nkhani zimene zatsala ndidzaziona ndikabwera.