1 Akorinto 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ntchito ziliponso zosiyanasiyana, koma pali Mulungu mmodzi amene amapereka mphamvu yogwirira ntchitozo kwa munthu aliyense.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:6 Nsanja ya Olonda,12/15/2011, ptsa. 24-25
6 Ntchito ziliponso zosiyanasiyana, koma pali Mulungu mmodzi amene amapereka mphamvu yogwirira ntchitozo kwa munthu aliyense.+