1 Akorinto 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 wina umamupatsa mphatso yochita ntchito zamphamvu,+ wina kunenera, wina kuzindikira mawu ouziridwa,+ wina kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana*+ ndiponso wina kumasulira zilankhulo.+
10 wina umamupatsa mphatso yochita ntchito zamphamvu,+ wina kunenera, wina kuzindikira mawu ouziridwa,+ wina kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana*+ ndiponso wina kumasulira zilankhulo.+