1 Akorinto 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tonsefe tinabatizidwa ndi mzimu umodzi kuti tikhale thupi limodzi. Kaya ndife Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena anthu aufulu, tonsefe tinalandira* mzimu umodzi. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:13 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 110
13 Tonsefe tinabatizidwa ndi mzimu umodzi kuti tikhale thupi limodzi. Kaya ndife Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena anthu aufulu, tonsefe tinalandira* mzimu umodzi.