-
1 Akorinto 12:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Koma ziwalo zathu zooneka bwino kale sizifunikira kuzisamalira choncho. Komabe Mulungu analumikiza bwino thupi lonse, kuti ziwalo zomwe zilibe ulemu wokwanira zizisamaliridwa kwambiri.
-