1 Akorinto 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipo chiwalo chimodzi chikavutika, ziwalo zina zonse zimavutika nacho limodzi,+ komanso chiwalo china chikalemekezedwa, ziwalo zina zonse zimasangalala nacho limodzi.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:26 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 19
26 Ndipo chiwalo chimodzi chikavutika, ziwalo zina zonse zimavutika nacho limodzi,+ komanso chiwalo china chikalemekezedwa, ziwalo zina zonse zimasangalala nacho limodzi.+