-
1 Akorinto 12:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Sikuti onse angakhale atumwi. Ndipo sizingatheke kuti onse akhale aneneri. Kodi onse angakhale aphunzitsi? Nanga onse angamachite ntchito zamphamvu?
-