-
1 Akorinto 13:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Pamene ndinali mwana, ndinkalankhula ngati mwana, kuganiza ngati mwana ndiponso kuona zinthu ngati mwana. Koma mmene ndakulamu, ndasiya zachibwana.
-