-
1 Akorinto 14:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Nʼzofanana ndi zipangizo zoimbira ngati chitoliro kapena zeze. Ngati maliridwe ake atangokhala amodzi osasinthasintha, kodi nʼzotheka kudziwa nyimbo imene ikuimbidwa ndi chitoliro kapena zezeyo?
-