-
1 Akorinto 14:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Nʼchimodzimodzinso ngati mukulankhula zosamveka. Kodi munthu angadziwe bwanji zimene mukunena? Mudzakhala kuti mukulankhula kwa mphepo.
-