-
1 Akorinto 14:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiye chofunika nʼchiyani? Ndiyenera kupemphera ndi mphatso ya mzimu, koma ndipempherenso ndi mawu omveka. Ndiimbe nyimbo zotamanda ndi mphatso ya mzimu, koma ndiimbenso ndi mawu omveka.
-